mwanawe cover art

Erstellt am Apr 25, 2026

Songtexte

(intro)
Willy k mw.

(Vers1)
Usalile tonthola.
Ndiwe fanizo lamwana olowelela.
Vuto chinyamata munachitengera.
Nkona mukadali opepera.
Because of you bambo mayi muzoophya adutsa.
Please maganizo oipa kwa makolo tachotsa .
Sangalole kholo kuti usadutse muzabwino.
Dziwa mayi ndi bambo ndi abwino.

(Corus)
Aipilenji lero makolo ako mwanawe.
Anakulera ukadali wakhanda nkukula aipilenji mwanawe.
Akanakhala oipa Mesa sukanabadwa nkukula nde lemekeza makolo.

(Vers2)
Esela kumvela bambo ndimai ako.
Please chonde osatengeka ndi anzako.
Poti pamene unkabadwa anzako kunalibeko.
Pakuti mulungu wako wachiwili ndimai ndibabo ako.
So better komwe uliko utabwera.kuti makolo ako akondere.
Osalitengera dziko.
Ukamaseka nalo limaseka.

(Corus)
Aipilenji lero makolo ako mwanawe.
Anakulera ukadali wakhanda nkukula aipilenji mwanawe.
Akanakhala oipa Mesa sukanabadwa nkukula nde lemekeza makolo.
Aipilenji lero makolo ako mwanawe.
Anakulera ukadali wakhanda nkukula aipilenji mwanawe.
Akanakhala oipa Mesa sukanabadwa nkukula nde lemekeza makolo.
ALEX BITON ON THE BEATS