Letra
(intro)
Mmmm afb kamakani,Mr makani music
(Corus)
Sindingakunamize vayiletii.
Sindingapeze wina kusiya iwe iii.
Ine ndimakukondaa wamvaa.
Sindingakonde wina zinazi ndizimbava.
Koma nawenso uzindikondaaa.
Ulonjeze zoti suzandisiya eee
(Vers1)
Ooo tabwela mkuuze mamiwee.
Zokusiya sindilabadaaa.
Payiwe ndabwela umvesese vayiletii.
Ndikufuna ndikuchengetele.
Undilonjeze suzandisiya vayileti.
Kunjaku kuli amuna anama.
Atha kukupusisa zoti amakukonda .
Ulimbe ntima chikondi ndiulendo.
Ulimbe ntima enawa ndimabubuda
Koma choti udziweee.
(Corus)
Sindingakunamize vayiletii.
Sindingapeze wina kusiya iwe iii.
Ine ndimakukondaa wamvaa.
Sindingakonde wina zinazi ndizimbava.
Koma nawenso uzindikondaaa.
Ulonjeze zoti suzandisiya eee.
(Vers2)
Tamvela vayileti ndakondapo joyii.
Ndisakubisile saziwa kukonda ee.
Kumupasa chikondi iye kukapasa wina.
Ine ndinali oluza iyeyo owina.
Komano akanaziwa .
Sibwenzi atandiswela ntima.
Mamuna anamukonda uja.
Anamusiya akondanso wina.
Ndiye ine ndakukonda vayiletii.
Sindikufuna wina azakupusise.
Koma choti udziweee.
(Corus)
Sindingakunamize vayiletii.
Sindingapeze wina kusiya iwe iii.
Ine ndimakukondaa wamvaa.
Sindingakonde wina zinazi ndizimbava.
Koma nawenso uzindikondaaa.
Ulonjeze zoti suzandisiya eee.
Sindingakunamize vayiletii.
Sindingapeze wina kusiya iwe iii.
Ine ndimakukondaa wamvaa.
Sindingakonde wina zinazi ndizimbava.
Koma nawenso uzindikondaaa.
Ulonjeze zoti suzandisiya eee
ALEX BITON ON THE BEATS.
Mmmm afb kamakani,Mr makani music
(Corus)
Sindingakunamize vayiletii.
Sindingapeze wina kusiya iwe iii.
Ine ndimakukondaa wamvaa.
Sindingakonde wina zinazi ndizimbava.
Koma nawenso uzindikondaaa.
Ulonjeze zoti suzandisiya eee
(Vers1)
Ooo tabwela mkuuze mamiwee.
Zokusiya sindilabadaaa.
Payiwe ndabwela umvesese vayiletii.
Ndikufuna ndikuchengetele.
Undilonjeze suzandisiya vayileti.
Kunjaku kuli amuna anama.
Atha kukupusisa zoti amakukonda .
Ulimbe ntima chikondi ndiulendo.
Ulimbe ntima enawa ndimabubuda
Koma choti udziweee.
(Corus)
Sindingakunamize vayiletii.
Sindingapeze wina kusiya iwe iii.
Ine ndimakukondaa wamvaa.
Sindingakonde wina zinazi ndizimbava.
Koma nawenso uzindikondaaa.
Ulonjeze zoti suzandisiya eee.
(Vers2)
Tamvela vayileti ndakondapo joyii.
Ndisakubisile saziwa kukonda ee.
Kumupasa chikondi iye kukapasa wina.
Ine ndinali oluza iyeyo owina.
Komano akanaziwa .
Sibwenzi atandiswela ntima.
Mamuna anamukonda uja.
Anamusiya akondanso wina.
Ndiye ine ndakukonda vayiletii.
Sindikufuna wina azakupusise.
Koma choti udziweee.
(Corus)
Sindingakunamize vayiletii.
Sindingapeze wina kusiya iwe iii.
Ine ndimakukondaa wamvaa.
Sindingakonde wina zinazi ndizimbava.
Koma nawenso uzindikondaaa.
Ulonjeze zoti suzandisiya eee.
Sindingakunamize vayiletii.
Sindingapeze wina kusiya iwe iii.
Ine ndimakukondaa wamvaa.
Sindingakonde wina zinazi ndizimbava.
Koma nawenso uzindikondaaa.
Ulonjeze zoti suzandisiya eee
ALEX BITON ON THE BEATS.