歌詞
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Aleluyah!
Ameh!
Koma Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh
Aleluyah
Ameh!
(chorus)
Inu Mulungu ndi Modzi
Ameh!
Mulungu ndi Modzi
Ameh!
Allah ndi Modzi
Ameh!
Allah ndi modzi
Ameh!
Ameh!
Ameh!
(Verse)
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Aleluyah!
Ameh!
Koma Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh
Aleluyah
Ameh!
(Final chorus)
Mulungu ndi Modzi
Ameh!
Ngakhale timasiyana zipembezo
Ameh!
Koma tose ndife Ana ake
Ameh!
Ndiye tisamanyozane
Ameh!
Tisamanyozelani Mipingo
Mpingo sukapulumutsa Muthu
Ameh!
Koma tchito zathu
Ndizomwe zikati Pulumutse
Kukafika ku Janah
Tchito zathu ndizomwe zikati pangitse
Kukafika ku Paladayizo
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Aleluyah!
Ameh!
Koma Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh
Aleluyah
Ameh!
(chorus)
Inu Mulungu ndi Modzi
Ameh!
Mulungu ndi Modzi
Ameh!
Allah ndi Modzi
Ameh!
Allah ndi modzi
Ameh!
Ameh!
Ameh!
(Verse)
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Aleluyah!
Ameh!
Koma Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh!
Asalamu alayikumu
Ameh
Aleluyah
Ameh!
(Final chorus)
Mulungu ndi Modzi
Ameh!
Ngakhale timasiyana zipembezo
Ameh!
Koma tose ndife Ana ake
Ameh!
Ndiye tisamanyozane
Ameh!
Tisamanyozelani Mipingo
Mpingo sukapulumutsa Muthu
Ameh!
Koma tchito zathu
Ndizomwe zikati Pulumutse
Kukafika ku Janah
Tchito zathu ndizomwe zikati pangitse
Kukafika ku Paladayizo