歌詞
(intro)
Wile keyi malawi, zamu again.
(Corus)
Give me one chance ndiyesenso please one chance.
Mmene mudalitsa enawo mbuye please nane one chance.
Cozi ndalila kokwana so teketeke ndiiphule.
(Vers1)
Am in strangles osaneneka.
And am trying kutakataka koma sizikutheka.
Moti ndukanika kupumula any time.
Please God even day imozi lokha ndiipasa fire cozi this life wanditopesa.
Ndipempha Inu chifukwa ndinu emwe muona ndikudziwa nkhawa zanga.
Podalisa enawo naneso chimodzi modzi.
Poti ndinu amene munadalitsa atapempha benty.
(Corus)
Give me one chance ndiesenso please one chance.

(Vers2)
Kugulu la azinzanga ndine ndekha amene zinthu sizikuyenda.
Pena ndimadabwa kuti ndipati pomwe anzanga anaponda.
But nditangomva zainu kuti muli kwathu kuno.
So ndawelamisa nkhope ndikupinda maondo.
Eya podalitsa anthu ena.
Ndikusintha nyengo za wena.Naneso chimodzi modzi.
Please give me one chance my God.

ALEX BITON ON THE BEATS