musamukakamize cover art

musamukakamize

L
Lex Petro

Creat pe apr. 24, 2026

Versuri

(intro)
Faya boyizi khlu,ine ndi yamyze bi zanyimbo adaa.
(Vers1)
Akulu akulu nkhalani chete,chete.
Ndikufuna ndikuwuzeni.
inali satade usiku.
Zomwe ndinamva zinandithesa mzelu.
Kunabwela makolo achibwenzi changa.
Eya panyumba panga.
Kuzandiuza kuti mwana wawo.
Akufuna amukwatilise.
Koma mwana wawoyo.
Ankawawuza .
Kukhala opanda ine sangakwanise.
Koma zomwe ankanena makolo akewo.
Ayi sanamvesese.
Pano mwana wawoyo akapita kubanja.
Ma wiki angapo abwelako.
Sanachite kusankha.
Makolo akewo ndiamene anamupangila chisankho.

(Corus)
Musamukakamize nayenso alindi chisankho chake.
Musamukakamize nayenso alindi chisankho chake.
Ngati asankha molakwika pasogolo azasintha,ya.
Ngati asankha molakwika pasogolo azasintha,ya.

(Vers2)
Makolo anu afuna chabwino ine ndilimommuno.
Koma zikazatha usazandiiwale uzandipeza mommuno.
Zavuta kumakolo Ana akufunana aaaa.
Ndikayiwale bwanji kwako kumzunana aaa.
Basi tivomeleze pakuti zatelo.
Ndati tivomeleze mkazi wanga debola.
Ngati uli nthiti yanga tizankhalila limodzi.
Ngati ineyo ndili wako chilichonse tizachita limodzi iii.

(Corus)
Musamukakamize nayenso alindi chisankho chake.
Musamukakamize nayenso alindi chisankho chake.
Ngati asankha molakwika pasogolo azasintha,ya.
Ngati asankha molakwika pasogolo azasintha,ya.
Musamukakamize nayenso alindi chisankho chake.
Musamukakamize nayenso alindi chisankho chake.
Ngati asankha molakwika pasogolo azasintha,ya.
Ngati asankha molakwika pasogolo azasintha,ya.
ALEX BITON ON THE BEARTS