mukhululuke cover art

mukhululuke

T
Teleza Junes

Créé le avr. 26, 2026

Paroles

(intro)
Mi nemu chifundo from chitimbe.

(Vers1)
Mkazi wanga takhala apapa tikambilane.
Eya tisanagone ifeyo timvane.
iwe ndi ine tinakondana.
Zaka zingapo zapitazo.
Koma makolo ako sakondwela ndi chikondi chathu.
Ife tinaganiza zongithawisanatu.
Ndye tibwelele kwa makolo tikawapepese.
Mwina akatimvesesa.

(Corus)
ifeyo ndi Ana anu eee.
Tikupempha mukhululukeee.
ifeyo ndi Ana anu eee.
Tikupempha mutimveseseee.
Paja munthu salakwila mtengo.
Chonde makolo mukhuluke.

(Vers2)
Chonde makolo mutimvesesekoo.
Zachikondi chathu musaletsetsenoo.
ine sindine sizinantole okuba.
Ndimangocheza ndi achina benati.
Chonde musatuluse mpeni.
Mwana wanu ndinamukonda zenizeni.
Chonde makolo musalimbe mtima khululukani.
ine ndiwabwino olo mufunse yamuze bi.

(Corus)
ifeyo ndi Ana anu eee.
Tikupempha mukhululukeee.
ifeyo ndi Ana anu eee.
Tikupempha mutimveseseee.
Paja munthu salakwila mtengo.
Chonde makolo mukhuluke.
ifeyo ndi Ana anu eee.
Tikupempha mukhululukeee.
ifeyo ndi Ana anu eee.
Tikupempha mutimveseseee.
Paja munthu salakwila mtengo.
Chonde makolo mukhuluke.
ALEX BITON ON THE BEATS